26 Anayamba kukhala kumeneko chifukwa Hesiboni unali mzinda wa Sihoni.+ Sihoni inali mfumu ya Aamori,+ ndipo iye ndiye anamenyana ndi mfumu ya Mowabu m’mbuyomo, n’kulanda dziko lonse limene linali m’manja mwake mpaka kuchigwa cha Arinoni.+
22 “Pamenepo munawapatsa maufumu+ ndi mitundu ya anthu ndipo munawagawira dzikolo chigawo ndi chigawo.+ Iwo anatenga dziko la Sihoni,+ dziko la mfumu ya Hesiboni+ ndi dziko la Ogi+ mfumu ya Basana.+