1 Mafumu 5:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kuwonjezera pa amenewa, panalinso akapitawo a nduna za Solomo+ oyang’anira ntchitoyo. Analipo akapitawo 3,300+ oyang’anira anthu amene anali kugwira ntchitoyo.
16 Kuwonjezera pa amenewa, panalinso akapitawo a nduna za Solomo+ oyang’anira ntchitoyo. Analipo akapitawo 3,300+ oyang’anira anthu amene anali kugwira ntchitoyo.