1 Samueli 10:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Choncho anthu anathamanga kukam’tenga kumeneko. Ataimirira pakati pa anthuwo, anali wam’tali kwambiri moti panalibe munthu aliyense amene anali kum’pitirira m’mapewa ake.+
23 Choncho anthu anathamanga kukam’tenga kumeneko. Ataimirira pakati pa anthuwo, anali wam’tali kwambiri moti panalibe munthu aliyense amene anali kum’pitirira m’mapewa ake.+