Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Maliko 6:41
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 41 Tsopano anatenga mitanda ya mkate isanu ija ndi nsomba ziwiri zija n’kuyang’ana kumwamba ndi kupempha dalitso.+ Kenako ananyemanyema+ mitanda ya mkateyo ndi kuipereka kwa ophunzira ake kuti aipereke kwa anthuwo, ndiponso anaduladula nsomba ziwirizo ndi kugawira anthu onsewo.

  • Luka 9:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Kenako anatenga mitanda ya mkate isanu ija ndi nsomba ziwiri zija ndipo anayang’ana kumwamba ndi kudalitsa chakudyacho. Kenako ananyemanyema mitanda ya mkate ndi nsombazo n’kupereka kwa ophunzira kuti apatse anthuwo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena