Oweruza 21:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Iwo anapitiriza kunena kuti: “Ndani mwa mafuko a Isiraeli amene sanabwere kwa Yehova ku Mizipa?”+ Pamenepo anaona kuti ku msasawo sikunabwere aliyense wochokera ku Yabesi-giliyadi+ kudzagwirizana ndi mpingowo. 1 Samueli 31:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Choncho, anthu okhala mumzinda wa Yabesi-giliyadi+ anamva zimene Afilisiti anamuchita Sauli.
8 Iwo anapitiriza kunena kuti: “Ndani mwa mafuko a Isiraeli amene sanabwere kwa Yehova ku Mizipa?”+ Pamenepo anaona kuti ku msasawo sikunabwere aliyense wochokera ku Yabesi-giliyadi+ kudzagwirizana ndi mpingowo.