1 Samueli 11:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndiyeno Nahasi Muamoni+ anapita kukamanga msasa kuti amenyane ndi mzinda wa Yabesi+ ku Giliyadi. Zitatero, amuna onse a ku Yabesi anauza Nahasi kuti: “Chita nafe pangano kuti tizikutumikira.”+
11 Ndiyeno Nahasi Muamoni+ anapita kukamanga msasa kuti amenyane ndi mzinda wa Yabesi+ ku Giliyadi. Zitatero, amuna onse a ku Yabesi anauza Nahasi kuti: “Chita nafe pangano kuti tizikutumikira.”+