1 Samueli 13:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Sauli anapitiriza kudikira kwa masiku 7 kufikira nthawi yoikidwiratu imene Samueli ananena.+ Koma Samueli sanafikebe ku Giligala, moti anthu anayamba kubalalika kum’siya Sauli.
8 Sauli anapitiriza kudikira kwa masiku 7 kufikira nthawi yoikidwiratu imene Samueli ananena.+ Koma Samueli sanafikebe ku Giligala, moti anthu anayamba kubalalika kum’siya Sauli.