Genesis 4:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Koma Zila anabereka Tubala-kaini, amene anali mmisiri wosula zipangizo zamtundu uliwonse, zamkuwa ndi zachitsulo.+ Ndipo mlongo wake wa Tubala-kaini anali Naama. Miyambo 27:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Chitsulo chimanola chitsulo chinzake. Momwemonso munthu amanola munthu mnzake.+
22 Koma Zila anabereka Tubala-kaini, amene anali mmisiri wosula zipangizo zamtundu uliwonse, zamkuwa ndi zachitsulo.+ Ndipo mlongo wake wa Tubala-kaini anali Naama.