Genesis 4:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Nayenso Seti anabereka mwana wamwamuna n’kumutcha dzina lakuti Enosi.+ Pa nthawi imeneyi, anthu anayamba kuitanira pa dzina la Yehova.+
26 Nayenso Seti anabereka mwana wamwamuna n’kumutcha dzina lakuti Enosi.+ Pa nthawi imeneyi, anthu anayamba kuitanira pa dzina la Yehova.+