Ekisodo 17:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndiyeno Aamaleki+ anabwera kudzamenyana ndi Isiraeli ku Refidimu.+ Numeri 24:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Tsopano Balamu ataona Amaleki, anapitiriza mawu ake a ndakatulo, kuti:+“Amaleki anali woyamba wa anthu a mitundu ina,+Koma chiwonongeko chake chidzakhaladi mapeto ake.”+ Deuteronomo 25:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “Muzikumbukira zimene Aamaleki anakuchitirani panjira pamene munali kutuluka mu Iguputo.+ Deuteronomo 25:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Iwo anakumana nanu panjira ndi kupha anthu oyenda movutika m’gulu lanu amene anali kumbuyo. Iwo anachita izi pamene munali olefuka ndi otopa ndipo sanaope Mulungu.+
20 Tsopano Balamu ataona Amaleki, anapitiriza mawu ake a ndakatulo, kuti:+“Amaleki anali woyamba wa anthu a mitundu ina,+Koma chiwonongeko chake chidzakhaladi mapeto ake.”+
18 Iwo anakumana nanu panjira ndi kupha anthu oyenda movutika m’gulu lanu amene anali kumbuyo. Iwo anachita izi pamene munali olefuka ndi otopa ndipo sanaope Mulungu.+