Yeremiya 48:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “Wotembereredwa ndi munthu wozengereza kugwira ntchito imene Yehova wamupatsa.+ Wotembereredwa ndi munthu wopewa kukhetsa magazi ndi lupanga lake.
10 “Wotembereredwa ndi munthu wozengereza kugwira ntchito imene Yehova wamupatsa.+ Wotembereredwa ndi munthu wopewa kukhetsa magazi ndi lupanga lake.