1 Samueli 13:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndiyeno zimene zinachitika n’zakuti, atangomaliza kupereka nsembe yopserezayo anaona Samueli akubwera. Choncho Sauli anatuluka kukakumana naye ndi kumulonjera.+
10 Ndiyeno zimene zinachitika n’zakuti, atangomaliza kupereka nsembe yopserezayo anaona Samueli akubwera. Choncho Sauli anatuluka kukakumana naye ndi kumulonjera.+