Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 47:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Kenako Yosefe anabweretsa bambo ake Yakobo n’kuwasonyeza kwa Farao. Ndipo Yakobo anadalitsa Farao.+

  • Rute 2:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Kenako Boazi anafika kuchokera ku Betelehemu ndipo anauza okololawo kuti: “Yehova akhale nanu.”+ Iwo anayankha mwa nthawi zonse kuti: “Yehova akudalitseni.”+

  • 1 Samueli 15:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Patapita nthawi Samueli anam’peza Sauli, ndipo Sauli anauza Samueli kuti: “Yehova akudalitseni.+ Ndachita zimene Yehova ananena.”+

  • 1 Samueli 25:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Izi zili choncho, mmodzi mwa anyamata a Nabala anauza Abigayeli, mkazi wa Nabala kuti: “Davide anatumiza nthumwi zake kuchokera m’chipululu kudzafunira zabwino mbuyanga, koma mbuyanga walalatira+ nthumwizo.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena