Miyambo 12:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Njira ya munthu wopusa imakhala yolondola m’maso mwake,+ koma womvera malangizo ndi wanzeru.+ Miyambo 18:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Woyamba kufotokoza mbali yake pa mlandu amaoneka ngati wolondola,+ koma mnzake amabwera n’kumufufuzafufuza.+ Miyambo 26:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kodi waona munthu wodziona ngati wanzeru m’maso mwake?+ Munthu wopusa ali ndi chiyembekezo chachikulu+ kuposa iyeyo.
17 Woyamba kufotokoza mbali yake pa mlandu amaoneka ngati wolondola,+ koma mnzake amabwera n’kumufufuzafufuza.+
12 Kodi waona munthu wodziona ngati wanzeru m’maso mwake?+ Munthu wopusa ali ndi chiyembekezo chachikulu+ kuposa iyeyo.