1 Samueli 17:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Davide anali wamng’ono kwambiri pa ana onse aamuna,+ ndipo ana atatu aakulu a Jese anatsatira Sauli.
14 Davide anali wamng’ono kwambiri pa ana onse aamuna,+ ndipo ana atatu aakulu a Jese anatsatira Sauli.