1 Samueli 16:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kenako Jese anaitana Shama+ kuti adutse, koma Samueli anati: “Yehova sanasankhenso ameneyu.” 2 Samueli 13:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Tsopano Aminoni anali ndi mnzake dzina lake Yehonadabu,+ mwana wa Simeya,+ m’bale wake wa Davide. Yehonadabu anali munthu wanzeru kwambiri.
3 Tsopano Aminoni anali ndi mnzake dzina lake Yehonadabu,+ mwana wa Simeya,+ m’bale wake wa Davide. Yehonadabu anali munthu wanzeru kwambiri.