1 Samueli 17:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndiyeno Mfilisiti uja anapitiriza kunena kuti: “Ine ndikutonza+ asilikali a Isiraeli lero. Ndipatseni mwamuna woti ndimenyane naye!”+
10 Ndiyeno Mfilisiti uja anapitiriza kunena kuti: “Ine ndikutonza+ asilikali a Isiraeli lero. Ndipatseni mwamuna woti ndimenyane naye!”+