1 Samueli 17:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Ndiyeno Davide anayamba kufunsa amuna amene anali ataimirira pafupi naye kuti: “Kodi munthu amene angakaphe Mfilisiti+ ameneyu ndi kuchotsa chitonzo pa Isiraeli+ amuchitira chiyani? Kodi Mfilisiti wosadulidwa+ ameneyu ndani kuti azinyoza+ asilikali a Mulungu wamoyo?”+ 2 Mafumu 19:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Kodi ndani amene iwe wamutonza+ ndi kumulankhula monyoza?+Ndipo ndani amene iwe wam’kwezera mawu,+Ndi kum’kwezera maso ako m’mwamba?+Ndi Woyera wa Isiraeli!+ Salimo 80:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mwachititsa kuti anthu oyandikana nafe azimenyana polimbirana ifeyo.+Ndipo adani athu akupitirizabe kutinyoza mmene akufunira.+
26 Ndiyeno Davide anayamba kufunsa amuna amene anali ataimirira pafupi naye kuti: “Kodi munthu amene angakaphe Mfilisiti+ ameneyu ndi kuchotsa chitonzo pa Isiraeli+ amuchitira chiyani? Kodi Mfilisiti wosadulidwa+ ameneyu ndani kuti azinyoza+ asilikali a Mulungu wamoyo?”+
22 Kodi ndani amene iwe wamutonza+ ndi kumulankhula monyoza?+Ndipo ndani amene iwe wam’kwezera mawu,+Ndi kum’kwezera maso ako m’mwamba?+Ndi Woyera wa Isiraeli!+
6 Mwachititsa kuti anthu oyandikana nafe azimenyana polimbirana ifeyo.+Ndipo adani athu akupitirizabe kutinyoza mmene akufunira.+