Salimo 71:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Inenso ndidzakutamandani ndi chipangizo cha zingwe,+Ndidzatamanda choonadi chanu, inu Mulungu.+Ndidzaimba nyimbo zokutamandani ndi zeze, Inu Woyera wa Isiraeli.+ Salimo 89:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pakuti chishango chathu ndi chochokera kwa Yehova,+Ndipo mfumu yathu ndi yochokera kwa Woyera wa Isiraeli.+ Yeremiya 51:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 “Pakuti Mulungu, Yehova wa makamu,+ sanasiye Isiraeli ndi Yuda+ kuti akhale mkazi wamasiye. Dziko la Akasidi lili ndi mlandu waukulu pamaso pa Woyera wa Isiraeli.+
22 Inenso ndidzakutamandani ndi chipangizo cha zingwe,+Ndidzatamanda choonadi chanu, inu Mulungu.+Ndidzaimba nyimbo zokutamandani ndi zeze, Inu Woyera wa Isiraeli.+
18 Pakuti chishango chathu ndi chochokera kwa Yehova,+Ndipo mfumu yathu ndi yochokera kwa Woyera wa Isiraeli.+
5 “Pakuti Mulungu, Yehova wa makamu,+ sanasiye Isiraeli ndi Yuda+ kuti akhale mkazi wamasiye. Dziko la Akasidi lili ndi mlandu waukulu pamaso pa Woyera wa Isiraeli.+