1 Samueli 14:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Choncho Yonatani anauza mtumiki wake womunyamulira zida uja kuti: “Tiye tiwolokere kumudzi wa amuna osadulidwawa.+ Pakuti mwina Yehova adzatithandiza, chifukwa palibe chimene chingalepheretse Yehova kupulumutsa anthu ake pogwiritsa ntchito anthu ambiri kapena ochepa.”+ 1 Samueli 18:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Pamenepo Sauli anati: “Amuna inu, mukauze Davide kuti, ‘Sikuti mfumu ikufuna ndalama za ukwati,+ koma ikufuna makungu 100 akunsonga + a Afilisiti, kuti ibwezere+ adani ake.’” Koma Sauli anali atakonza chiwembu kuti Davide aphedwe ndi Afilisiti.
6 Choncho Yonatani anauza mtumiki wake womunyamulira zida uja kuti: “Tiye tiwolokere kumudzi wa amuna osadulidwawa.+ Pakuti mwina Yehova adzatithandiza, chifukwa palibe chimene chingalepheretse Yehova kupulumutsa anthu ake pogwiritsa ntchito anthu ambiri kapena ochepa.”+
25 Pamenepo Sauli anati: “Amuna inu, mukauze Davide kuti, ‘Sikuti mfumu ikufuna ndalama za ukwati,+ koma ikufuna makungu 100 akunsonga + a Afilisiti, kuti ibwezere+ adani ake.’” Koma Sauli anali atakonza chiwembu kuti Davide aphedwe ndi Afilisiti.