Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mafumu 18:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Musalole kuti Hezekiya akuchititseni kudalira Yehova,+ pokuuzani kuti: “Mosakayikira Yehova atilanditsa,+ ndipo mzindawu superekedwa m’manja mwa mfumu ya Asuri.”+

  • Yesaya 10:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Pakuti iye wanena kuti, ‘Ndi mphamvu za dzanja langa ndiponso ndi nzeru zanga, ndidzachitapo kanthu+ chifukwa ndine wodziwa zinthu. Ndidzachotsa malire a mitundu ya anthu,+ ndipo zinthu zimene anasunga ndidzazilanda.+ Monga munthu wamphamvu, ndidzagwetsa anthu okhala mmenemo.+

  • Yesaya 14:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Iweyo wanena mumtima mwako kuti, ‘Ndikwera kumwamba.+ Ndikweza mpando wanga wachifumu+ pamwamba pa nyenyezi+ za Mulungu. Ndikhala paphiri lokumanapo+ kumapeto kwenikweni kwa madera a kumpoto.+

  • Mateyu 23:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Aliyense wodzikweza adzatsitsidwa,+ koma aliyense wodzichepetsa adzakwezedwa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena