Yesaya 47:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Iwe unali kunena kuti: “Ine ndidzakhala Dona mpaka kalekale,+ mpaka muyaya.” Sunaganizire zinthu izi mumtima mwako ndipo sunaganizire kuti zidzatha bwanji.+ Danieli 4:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Mfumuyo inali kunena kuti:+ “Kodi uyu si Babulo Wamkulu amene ine ndamanga ndi mphamvu zanga zazikulu+ ndiponso ndi ulemerero wanga waukulu ndi cholinga chakuti kukhale nyumba yachifumu?”+
7 Iwe unali kunena kuti: “Ine ndidzakhala Dona mpaka kalekale,+ mpaka muyaya.” Sunaganizire zinthu izi mumtima mwako ndipo sunaganizire kuti zidzatha bwanji.+
30 Mfumuyo inali kunena kuti:+ “Kodi uyu si Babulo Wamkulu amene ine ndamanga ndi mphamvu zanga zazikulu+ ndiponso ndi ulemerero wanga waukulu ndi cholinga chakuti kukhale nyumba yachifumu?”+