Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 2:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 M’masiku otsiriza,+ phiri la nyumba+ ya Yehova lidzakhazikika pamwamba pa nsonga za mapiri,+ ndipo lidzakwezedwa pamwamba pa mapiri ang’onoang’ono.+ Mitundu yonse idzakhamukira kumeneko.+

  • Yesaya 24:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Mwezi wathunthu wachita manyazi. Dzuwa lowala lachitanso manyazi,+ pakuti Yehova wa makamu wakhala mfumu+ yaulemerero m’phiri la Ziyoni+ ndi mu Yerusalemu, pamaso pa anthu ake achikulire.+

  • Yoweli 3:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Pamenepo anthu inu mudzadziwa kuti ine ndine Yehova Mulungu wanu,+ amene ndimakhala mu Ziyoni, phiri langa lopatulika.+ Yerusalemu adzakhala malo anga opatulika,+ ndipo alendo sadzadutsanso mmenemo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena