Obadiya 16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pakuti mmene anthu inu munali kumwera vinyo paphiri langa loyera, ndi mmenenso mitundu ina yonse ya anthu izidzamwera mkwiyo wanga ngati vinyo nthawi zonse.+ Iwo adzamwa ndi kugugudiza mkwiyo wanga, ndipo zidzakhala ngati iwo kunalibe. Zekariya 8:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Yehova wanena kuti, ‘Ndidzabwerera ku Ziyoni+ ndipo ndidzakhala mu Yerusalemu.+ Yerusalemu adzatchedwadi mzinda wa choonadi+ ndi phiri loyera+ la Yehova+ wa makamu.’”
16 Pakuti mmene anthu inu munali kumwera vinyo paphiri langa loyera, ndi mmenenso mitundu ina yonse ya anthu izidzamwera mkwiyo wanga ngati vinyo nthawi zonse.+ Iwo adzamwa ndi kugugudiza mkwiyo wanga, ndipo zidzakhala ngati iwo kunalibe.
3 “Yehova wanena kuti, ‘Ndidzabwerera ku Ziyoni+ ndipo ndidzakhala mu Yerusalemu.+ Yerusalemu adzatchedwadi mzinda wa choonadi+ ndi phiri loyera+ la Yehova+ wa makamu.’”