Danieli 2:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Pamenepo chitsulo, dongo, mkuwa, siliva ndi golide, zonsezi zinaphwanyikaphwanyika ndipo zinakhala ngati mankhusu* apamalo opunthirapo mbewu+ m’chilimwe. Mphepo inaziuluza moti sizinaonekenso.+ Koma mwala umene unamenya chifanizirocho unakhala phiri lalikulu ndipo linadzaza dziko lonse lapansi.+ Zekariya 8:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Yehova wanena kuti, ‘Ndidzabwerera ku Ziyoni+ ndipo ndidzakhala mu Yerusalemu.+ Yerusalemu adzatchedwadi mzinda wa choonadi+ ndi phiri loyera+ la Yehova+ wa makamu.’” Aheberi 12:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Koma m’malomwake, inu mwafika kuphiri la Ziyoni+ ndi mzinda+ wa Mulungu wamoyo, Yerusalemu wakumwamba,+ kumene kuli angelo miyandamiyanda,*+ Chivumbulutso 21:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Choncho, mu mphamvu ya mzimu, ananditengera kuphiri lalikulu ndi lalitali,+ ndipo anandionetsa mzinda woyera,+ Yerusalemu, ukutsika kuchokera kumwamba kwa Mulungu,+
35 Pamenepo chitsulo, dongo, mkuwa, siliva ndi golide, zonsezi zinaphwanyikaphwanyika ndipo zinakhala ngati mankhusu* apamalo opunthirapo mbewu+ m’chilimwe. Mphepo inaziuluza moti sizinaonekenso.+ Koma mwala umene unamenya chifanizirocho unakhala phiri lalikulu ndipo linadzaza dziko lonse lapansi.+
3 “Yehova wanena kuti, ‘Ndidzabwerera ku Ziyoni+ ndipo ndidzakhala mu Yerusalemu.+ Yerusalemu adzatchedwadi mzinda wa choonadi+ ndi phiri loyera+ la Yehova+ wa makamu.’”
22 Koma m’malomwake, inu mwafika kuphiri la Ziyoni+ ndi mzinda+ wa Mulungu wamoyo, Yerusalemu wakumwamba,+ kumene kuli angelo miyandamiyanda,*+
10 Choncho, mu mphamvu ya mzimu, ananditengera kuphiri lalikulu ndi lalitali,+ ndipo anandionetsa mzinda woyera,+ Yerusalemu, ukutsika kuchokera kumwamba kwa Mulungu,+