Mika 4:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 M’masiku otsiriza,+ phiri+ la nyumba+ ya Yehova lidzakhazikika pamwamba pa nsonga za mapiri, ndipo lidzakwezedwa pamwamba pa mapiri ang’onoang’ono.+ Mitundu ya anthu idzakhamukira kumeneko.+
4 M’masiku otsiriza,+ phiri+ la nyumba+ ya Yehova lidzakhazikika pamwamba pa nsonga za mapiri, ndipo lidzakwezedwa pamwamba pa mapiri ang’onoang’ono.+ Mitundu ya anthu idzakhamukira kumeneko.+