Salimo 86:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mitundu yonse imene munapanga idzabwera kwa inu,+Ndipo idzagwada pamaso panu, inu Yehova,+Ndi kulemekeza dzina lanu.+ Yesaya 60:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mitundu ya anthu idzatsata kuwala kwako,+ ndipo mafumu+ adzatsata kunyezimira kwako.+ Chivumbulutso 15:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kodi ndani sadzakuopani,+ inu Yehova?+ Ndani sadzalemekeza dzina lanu?+ Pakuti inu nokha ndinu wokhulupirika.+ Mitundu yonse ya anthu idzabwera kudzalambira pamaso panu,+ chifukwa malamulo anu olungama aonekera.”+
9 Mitundu yonse imene munapanga idzabwera kwa inu,+Ndipo idzagwada pamaso panu, inu Yehova,+Ndi kulemekeza dzina lanu.+
4 Kodi ndani sadzakuopani,+ inu Yehova?+ Ndani sadzalemekeza dzina lanu?+ Pakuti inu nokha ndinu wokhulupirika.+ Mitundu yonse ya anthu idzabwera kudzalambira pamaso panu,+ chifukwa malamulo anu olungama aonekera.”+