Salimo 86:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mitundu yonse ya anthu imene munapangaIdzabwera nʼkudzagwada pamaso panu, inu Yehova,+Ndipo idzalemekeza dzina lanu.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 86:9 Nsanja ya Olonda,12/15/1992, tsa. 13
9 Mitundu yonse ya anthu imene munapangaIdzabwera nʼkudzagwada pamaso panu, inu Yehova,+Ndipo idzalemekeza dzina lanu.+