Salimo 22:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Adzafika ndi kunena za chilungamo chake,+Adzauza anthu amene adzabadwe kuti iye ndiye wachita zimenezi.+ Yesaya 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 M’masiku otsiriza,+ phiri la nyumba+ ya Yehova lidzakhazikika pamwamba pa nsonga za mapiri,+ ndipo lidzakwezedwa pamwamba pa mapiri ang’onoang’ono.+ Mitundu yonse idzakhamukira kumeneko.+ Yesaya 43:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Bweretsa aliyense amene amatchedwa ndi dzina langa,+ amene ndinamulenga chifukwa cha ulemerero wanga,+ amene ndinamuumba ndiponso amene ndinamupanga.’+ Chivumbulutso 15:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kodi ndani sadzakuopani,+ inu Yehova?+ Ndani sadzalemekeza dzina lanu?+ Pakuti inu nokha ndinu wokhulupirika.+ Mitundu yonse ya anthu idzabwera kudzalambira pamaso panu,+ chifukwa malamulo anu olungama aonekera.”+
31 Adzafika ndi kunena za chilungamo chake,+Adzauza anthu amene adzabadwe kuti iye ndiye wachita zimenezi.+
2 M’masiku otsiriza,+ phiri la nyumba+ ya Yehova lidzakhazikika pamwamba pa nsonga za mapiri,+ ndipo lidzakwezedwa pamwamba pa mapiri ang’onoang’ono.+ Mitundu yonse idzakhamukira kumeneko.+
7 Bweretsa aliyense amene amatchedwa ndi dzina langa,+ amene ndinamulenga chifukwa cha ulemerero wanga,+ amene ndinamuumba ndiponso amene ndinamupanga.’+
4 Kodi ndani sadzakuopani,+ inu Yehova?+ Ndani sadzalemekeza dzina lanu?+ Pakuti inu nokha ndinu wokhulupirika.+ Mitundu yonse ya anthu idzabwera kudzalambira pamaso panu,+ chifukwa malamulo anu olungama aonekera.”+