8 Pamenepo Ahazi anatenga siliva ndi golide amene anali panyumba ya Yehova+ ndiponso wochokera pa chuma cha m’nyumba ya mfumu, n’kuzitumiza kwa mfumu ya Asuri ngati chiphuphu.+
16 Pamenepo Hezekiya mfumu ya Yuda anachotsa zitseko za kachisi wa Yehova+ ndi mafelemu ake, zimene iye anazikuta+ ndi golide, n’kupereka golideyo kwa mfumu ya Asuri.