2 Mafumu 18:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Choncho Rabisake+ anawauza kuti: “Mukauze Hezekiya kuti, ‘Mfumu yaikulu,+ mfumu ya Asuri yanena kuti: “Kodi ukudalira chiyani?+ 2 Mafumu 19:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Kodi ndani amene iwe wamutonza+ ndi kumulankhula monyoza?+Ndipo ndani amene iwe wam’kwezera mawu,+Ndi kum’kwezera maso ako m’mwamba?+Ndi Woyera wa Isiraeli!+ Salimo 11:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ine ndathawira kwa Yehova.+Kodi mulibe mantha? Mukundiuza kuti:“Thawirani kumapiri anu ngati mbalame!+ Salimo 22:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Anadzipereka kwa Yehova.+ Amupulumutse Iyeyo!+Ngati Mulungu amamukonda, amulanditse!”+
19 Choncho Rabisake+ anawauza kuti: “Mukauze Hezekiya kuti, ‘Mfumu yaikulu,+ mfumu ya Asuri yanena kuti: “Kodi ukudalira chiyani?+
22 Kodi ndani amene iwe wamutonza+ ndi kumulankhula monyoza?+Ndipo ndani amene iwe wam’kwezera mawu,+Ndi kum’kwezera maso ako m’mwamba?+Ndi Woyera wa Isiraeli!+
11 Ine ndathawira kwa Yehova.+Kodi mulibe mantha? Mukundiuza kuti:“Thawirani kumapiri anu ngati mbalame!+