2 Mafumu 19:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 “‘N’chifukwa chake Yehova wanena izi zokhudza mfumu ya Asuri:+ “Sadzalowa mumzinda uno,+ kapena kuponyamo muvi,+ kapena kufikamo ndi chishango, kapenanso kumanga chiunda chomenyerapo nkhondo* pafupi ndi mpanda wa mzindawu atauzungulira.+ Yesaya 36:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Musalole kuti Hezekiya akuchititseni kudalira Yehova,+ pokuuzani kuti: “Mosakayikira Yehova atilanditsa,+ ndipo mzindawu superekedwa m’manja mwa mfumu ya Asuri.”+
32 “‘N’chifukwa chake Yehova wanena izi zokhudza mfumu ya Asuri:+ “Sadzalowa mumzinda uno,+ kapena kuponyamo muvi,+ kapena kufikamo ndi chishango, kapenanso kumanga chiunda chomenyerapo nkhondo* pafupi ndi mpanda wa mzindawu atauzungulira.+
15 Musalole kuti Hezekiya akuchititseni kudalira Yehova,+ pokuuzani kuti: “Mosakayikira Yehova atilanditsa,+ ndipo mzindawu superekedwa m’manja mwa mfumu ya Asuri.”+