2 Mafumu 19:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “Amuna inu mukamuuze Hezekiya mfumu ya Yuda kuti, ‘Usalole Mulungu wako amene ukum’dalira kuti akunamize,+ ponena kuti: “Yerusalemu+ saperekedwa m’manja mwa mfumu ya Asuri.”+ 2 Mafumu 19:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Kodi ndani amene iwe wamutonza+ ndi kumulankhula monyoza?+Ndipo ndani amene iwe wam’kwezera mawu,+Ndi kum’kwezera maso ako m’mwamba?+Ndi Woyera wa Isiraeli!+ Salimo 11:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ine ndathawira kwa Yehova.+Kodi mulibe mantha? Mukundiuza kuti:“Thawirani kumapiri anu ngati mbalame!+ Salimo 22:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Anadzipereka kwa Yehova.+ Amupulumutse Iyeyo!+Ngati Mulungu amamukonda, amulanditse!”+
10 “Amuna inu mukamuuze Hezekiya mfumu ya Yuda kuti, ‘Usalole Mulungu wako amene ukum’dalira kuti akunamize,+ ponena kuti: “Yerusalemu+ saperekedwa m’manja mwa mfumu ya Asuri.”+
22 Kodi ndani amene iwe wamutonza+ ndi kumulankhula monyoza?+Ndipo ndani amene iwe wam’kwezera mawu,+Ndi kum’kwezera maso ako m’mwamba?+Ndi Woyera wa Isiraeli!+
11 Ine ndathawira kwa Yehova.+Kodi mulibe mantha? Mukundiuza kuti:“Thawirani kumapiri anu ngati mbalame!+