Salimo 71:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Inu Mulungu, musakhale kutali ndi ine.+Inu Mulungu wanga, fulumirani kundithandiza.+ Salimo 125:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 125 Okhulupirira Yehova+Ali ngati phiri la Ziyoni,+ limene silingagwedezeke, koma lidzakhalapo mpaka kalekale.+
125 Okhulupirira Yehova+Ali ngati phiri la Ziyoni,+ limene silingagwedezeke, koma lidzakhalapo mpaka kalekale.+