Yesaya 37:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 “‘Chotero Yehova wanena izi zokhudza mfumu ya Asuri:+ “Sadzalowa mumzinda uno,+ kapena kuponyamo muvi, kapena kufikamo ndi chishango, kapenanso kumanga chiunda chomenyerapo nkhondo pafupi ndi mpanda wa mzindawu atauzungulira.”’+
33 “‘Chotero Yehova wanena izi zokhudza mfumu ya Asuri:+ “Sadzalowa mumzinda uno,+ kapena kuponyamo muvi, kapena kufikamo ndi chishango, kapenanso kumanga chiunda chomenyerapo nkhondo pafupi ndi mpanda wa mzindawu atauzungulira.”’+