2 Mafumu 19:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 “‘N’chifukwa chake Yehova wanena izi zokhudza mfumu ya Asuri:+ “Sadzalowa mumzinda uno,+ kapena kuponyamo muvi,+ kapena kufikamo ndi chishango, kapenanso kumanga chiunda chomenyerapo nkhondo* pafupi ndi mpanda wa mzindawu atauzungulira.+
32 “‘N’chifukwa chake Yehova wanena izi zokhudza mfumu ya Asuri:+ “Sadzalowa mumzinda uno,+ kapena kuponyamo muvi,+ kapena kufikamo ndi chishango, kapenanso kumanga chiunda chomenyerapo nkhondo* pafupi ndi mpanda wa mzindawu atauzungulira.+