20 Taonani Ziyoni,+ tauni yathu yochitiramo zikondwerero.+ Maso anu adzaona Yerusalemu, amene ndi malo okhala aphee, opanda chosokoneza chilichonse. Iye ndi hema woti palibe amene adzamuchotse.+ Zikhomo zake sizidzazulidwa ndipo zingwe zake sizidzaduka.+