2 Mafumu 19:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Awa ndi mawu otsutsana naye amene Yehova wanena:“Namwali, mwana wamkazi wa Ziyoni, wakunyoza+ ndipo wakuseka.+Kumbuyo kwako, mwana wamkazi wa Yerusalemu+ wakupukusira mutu.+ Salimo 132:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Yehova wasankha Ziyoni,+Ndipo amafunitsitsa kuti akhale malo ake okhalamo. Iye amati:+ Yesaya 10:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Chotero Yehova wa makamu, Ambuye Wamkulu Koposa,+ wanena kuti: “Anthu anga amene mukukhala m’Ziyoni,+ musachite mantha chifukwa cha Msuri amene anali kukukwapulani ndi chikwapu+ ndiponso kukumenyani ndi ndodo, ngati mmene Iguputo anali kuchitira.+
21 Awa ndi mawu otsutsana naye amene Yehova wanena:“Namwali, mwana wamkazi wa Ziyoni, wakunyoza+ ndipo wakuseka.+Kumbuyo kwako, mwana wamkazi wa Yerusalemu+ wakupukusira mutu.+
24 Chotero Yehova wa makamu, Ambuye Wamkulu Koposa,+ wanena kuti: “Anthu anga amene mukukhala m’Ziyoni,+ musachite mantha chifukwa cha Msuri amene anali kukukwapulani ndi chikwapu+ ndiponso kukumenyani ndi ndodo, ngati mmene Iguputo anali kuchitira.+