1 Samueli 22:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Iye anakanthanso ndi lupanga Nobu,+ mzinda wa ansembe. Anapha amuna, akazi, ana aang’ono ndi ana oyamwa, komanso ng’ombe zamphongo, abulu ndi nkhosa. Nehemiya 11:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 ku Anatoti,+ Nobu,+ Ananiya,
19 Iye anakanthanso ndi lupanga Nobu,+ mzinda wa ansembe. Anapha amuna, akazi, ana aang’ono ndi ana oyamwa, komanso ng’ombe zamphongo, abulu ndi nkhosa.