1 Samueli 21:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Kenako Davide anafika ku Nobu+ kwa Ahimeleki wansembe. Ahimeleki+ ataona Davide anayamba kunjenjemera, ndipo anam’funsa kuti: “N’chifukwa chiyani uli wekha popanda munthu wina?”+ 1 Samueli 22:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pamenepo Doegi,+ Mwedomu, amene anali mkulu wa atumiki a Sauli anayankha kuti: “Ineyo ndinaona mwana wa Jese atabwera ku Nobu kwa Ahimeleki,+ mwana wa Ahitubu.+
21 Kenako Davide anafika ku Nobu+ kwa Ahimeleki wansembe. Ahimeleki+ ataona Davide anayamba kunjenjemera, ndipo anam’funsa kuti: “N’chifukwa chiyani uli wekha popanda munthu wina?”+
9 Pamenepo Doegi,+ Mwedomu, amene anali mkulu wa atumiki a Sauli anayankha kuti: “Ineyo ndinaona mwana wa Jese atabwera ku Nobu kwa Ahimeleki,+ mwana wa Ahitubu.+