1 Samueli 22:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Iye anakanthanso ndi lupanga Nobu,+ mzinda wa ansembe. Anapha amuna, akazi, ana aang’ono ndi ana oyamwa, komanso ng’ombe zamphongo, abulu ndi nkhosa. Nehemiya 11:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 ku Anatoti,+ Nobu,+ Ananiya, Yesaya 10:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Kukadali masana, iye aima ku Nobu.+ Ndi dzanja lake, iye akuopseza phiri la mwana wamkazi wa Ziyoni, phiri limene pali Yerusalemu.+
19 Iye anakanthanso ndi lupanga Nobu,+ mzinda wa ansembe. Anapha amuna, akazi, ana aang’ono ndi ana oyamwa, komanso ng’ombe zamphongo, abulu ndi nkhosa.
32 Kukadali masana, iye aima ku Nobu.+ Ndi dzanja lake, iye akuopseza phiri la mwana wamkazi wa Ziyoni, phiri limene pali Yerusalemu.+