Salimo 74:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kumbukirani izi: Inu Yehova, mdani wakuchitirani mopanda ulemu,+Ndipo anthu opusa anyoza dzina lanu.+ Salimo 74:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Nyamukani inu Mulungu, weruzani mlandu wanu.+Kumbukirani mmene munthu wopusa wakunyozerani tsiku lonse.+ Salimo 79:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Bwezerani anthu oyandikana nafe mwa kuwatsanulira chitonzo pachifuwa pawo maulendo 7,+Inu Yehova, muwabwezere chitonzo chimene anachita pa inu.+
18 Kumbukirani izi: Inu Yehova, mdani wakuchitirani mopanda ulemu,+Ndipo anthu opusa anyoza dzina lanu.+
22 Nyamukani inu Mulungu, weruzani mlandu wanu.+Kumbukirani mmene munthu wopusa wakunyozerani tsiku lonse.+
12 Bwezerani anthu oyandikana nafe mwa kuwatsanulira chitonzo pachifuwa pawo maulendo 7,+Inu Yehova, muwabwezere chitonzo chimene anachita pa inu.+