Salimo 9:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Nyamukani, inu Yehova! Munthu asakuposeni mphamvu.+Anthu a mitundu ina aweruzidwe pamaso panu.+