1 Samueli 17:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Ndiyeno Davide anawonjezera kuti: “Yehova amene anandilanditsa m’kamwa mwa mkango ndi m’kamwa mwa chimbalangondo andilanditsanso m’manja mwa Mfilisiti ameneyu.”+ Pamenepo Sauli anauza Davide kuti: “Pita, ndipo Yehova akhale nawe.”+
37 Ndiyeno Davide anawonjezera kuti: “Yehova amene anandilanditsa m’kamwa mwa mkango ndi m’kamwa mwa chimbalangondo andilanditsanso m’manja mwa Mfilisiti ameneyu.”+ Pamenepo Sauli anauza Davide kuti: “Pita, ndipo Yehova akhale nawe.”+