1 Samueli 14:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Choncho Yonatani anauza mtumiki wake womunyamulira zida uja kuti: “Tiye tiwolokere kumudzi wa amuna osadulidwawa.+ Pakuti mwina Yehova adzatithandiza, chifukwa palibe chimene chingalepheretse Yehova kupulumutsa anthu ake pogwiritsa ntchito anthu ambiri kapena ochepa.”+ Salimo 97:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Inu okonda Yehova+ danani nacho choipa.+Iye amateteza moyo wa anthu ake okhulupirika.+Amawalanditsa m’manja mwa anthu oipa.+ Salimo 124:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Thandizo lathu lili m’dzina la Yehova,+Wopanga kumwamba ndi dziko lapansi.”+
6 Choncho Yonatani anauza mtumiki wake womunyamulira zida uja kuti: “Tiye tiwolokere kumudzi wa amuna osadulidwawa.+ Pakuti mwina Yehova adzatithandiza, chifukwa palibe chimene chingalepheretse Yehova kupulumutsa anthu ake pogwiritsa ntchito anthu ambiri kapena ochepa.”+
10 Inu okonda Yehova+ danani nacho choipa.+Iye amateteza moyo wa anthu ake okhulupirika.+Amawalanditsa m’manja mwa anthu oipa.+