Deuteronomo 20:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 kuti, ‘Mverani Aisiraeli inu. Lero mukuyandikira adani anu kuti mumenyane nawo. Mitima yanu isachite mantha.+ Musaope ndipo musathawe mwamantha kapena kunjenjemera chifukwa cha iwo,+ Salimo 27:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ngakhale gulu lankhondo litamanga msasa kuti lindiukire,+Mtima wanga sudzachita mantha.+Ngakhale nkhondo yolimbana ndi ine itayambika,+Pameneponso ndidzadalira Mulungu.+
3 kuti, ‘Mverani Aisiraeli inu. Lero mukuyandikira adani anu kuti mumenyane nawo. Mitima yanu isachite mantha.+ Musaope ndipo musathawe mwamantha kapena kunjenjemera chifukwa cha iwo,+
3 Ngakhale gulu lankhondo litamanga msasa kuti lindiukire,+Mtima wanga sudzachita mantha.+Ngakhale nkhondo yolimbana ndi ine itayambika,+Pameneponso ndidzadalira Mulungu.+