Salimo 27:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Yehova ndiye kuwala+ kwanga ndi chipulumutso changa.+Ndingaopenso ndani?+Yehova ndiye malo a chitetezo cha moyo wanga.+Ndingachitenso mantha ndi ndani?+ Miyambo 28:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Anthu oipa amathawa popanda wowathamangitsa,+ koma olungama ali ngati mkango wamphamvu umene umakhala wolimba mtima.+
27 Yehova ndiye kuwala+ kwanga ndi chipulumutso changa.+Ndingaopenso ndani?+Yehova ndiye malo a chitetezo cha moyo wanga.+Ndingachitenso mantha ndi ndani?+
28 Anthu oipa amathawa popanda wowathamangitsa,+ koma olungama ali ngati mkango wamphamvu umene umakhala wolimba mtima.+