1 Samueli 17:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Koma Sauli ndi amuna a Isiraeli anasonkhana pamodzi n’kumanga msasa m’chigwa cha Ela,+ ndipo anafola mwa dongosolo lomenyera nkhondo kuti amenyane ndi Afilisiti. 1 Samueli 17:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Pa nthawiyi, Sauli, ana a Jese ndi amuna ena onse a Isiraeli anali m’chigwa cha Ela+ kuti amenyane ndi Afilisiti.+
2 Koma Sauli ndi amuna a Isiraeli anasonkhana pamodzi n’kumanga msasa m’chigwa cha Ela,+ ndipo anafola mwa dongosolo lomenyera nkhondo kuti amenyane ndi Afilisiti.
19 Pa nthawiyi, Sauli, ana a Jese ndi amuna ena onse a Isiraeli anali m’chigwa cha Ela+ kuti amenyane ndi Afilisiti.+