1 Samueli 30:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndiyeno Davide anawakantha ndi kuwawononga, kuyambira m’bandakucha kufikira madzulo. Palibe aliyense wa iwo amene anathawa,+ kupatulapo anyamata 400 amene anakwera ngamila n’kuthawa.
17 Ndiyeno Davide anawakantha ndi kuwawononga, kuyambira m’bandakucha kufikira madzulo. Palibe aliyense wa iwo amene anathawa,+ kupatulapo anyamata 400 amene anakwera ngamila n’kuthawa.