2 Samueli 9:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mefiboseti atamva zimenezi anawerama mpaka nkhope yake pansi ndipo anati: “Kodi ine mtumiki wanu ndine ndani kuti mukumbukire galu wakufa+ ngati ine?”
8 Mefiboseti atamva zimenezi anawerama mpaka nkhope yake pansi ndipo anati: “Kodi ine mtumiki wanu ndine ndani kuti mukumbukire galu wakufa+ ngati ine?”